Africa-Press – Malawi. Atatha kugwira ntchito zina zaboma mchigawo chakumwera, wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Michael Usi Lachinayi pa 20 February 2025 analankhula ndi khamu la anthu omwe anasonkhana ku nyumba ya boma ya Mudi mumzinda wa Blantyre.
For More News And Analysis About Malawi Follow Africa-Press





